Chichewa

Moto olusa waononga msika wa Zigwagwa ku Mzuzu

Moto wolusa watentha mbali imodzi ya msika wa Zigwagwa mu mzinda wa Mzuzu ndipo katundu wankhani-nkhani wawonongeka.

'Fredokiss tamumanga chifukwa anasokoneza ndalama zamalonda,'...

Katswiri oyimba chamba cha 'Hip-hop' Penjani Kalua yemwe amadziwikanso ndi dzina la Fredokiss ali mchitokosi chapolisi mumzinda wa...